National Anthems & Patriotic Songs "Malawian National Anthem - Mulungu dalitsa Malaŵi" Слова пісні

Переклад:enptruto

Malawian National Anthem - Mulungu dalitsa Malaŵi

Mlungu dalitsani Malaŵi,Mumsunge m'mtendere.Gonjetsani adani onse,Njala, nthenda, nsanje.Lunzitsani mitima yathu,Kuti tisaope.Mdalitse Mtsogoleri nafe,Ndi Mayi Malaŵi.

Malaŵi ndziko lokongola,La chonde ndi ufulu,Nyanja ndi mphepo ya m'mapiri,Ndithudi tadala.Zigwa, mapiri, nthaka, dzinthu,N'mphatso zaulere.Nkhalango, madambo abwino.Ngwokoma Malaŵi.

O Ufulu tigwirizane,Kukweza Malaŵi.Ndi chikondi, khama, kumvera,Timutumikire.Pa nkhondo nkana pa mtendere,Cholinga n'chimodzi.Mayi, bambo, tidzipereke,Pokweza Malaŵi.

Тут можна знайти слова пісні Malawian National Anthem - Mulungu dalitsa Malaŵi National Anthems & Patriotic Songs. Чи текст вірша Malawian National Anthem - Mulungu dalitsa Malaŵi. National Anthems & Patriotic Songs Malawian National Anthem - Mulungu dalitsa Malaŵi текст.